Deuteronomo 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu a mtundu wanu obalalitsidwawo akadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani ndi kukutengani kumeneko.+ Zekariya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Fulumirani! Fulumirani anthu inu! Thawani m’dziko la kumpoto,”+ watero Yehova. “Anthu inu, ndinakubalalitsirani kutali kumbali zonse za dziko lapansi,”*+ watero Yehova. Mateyu 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwamphamvu kwa lipenga,+ ndipo adzasonkhanitsa osankhidwa ake+ kuchokera kumphepo zinayi,+ kuchokera kumalekezero a m’mlengalenga mpaka kumalekezero ena.
4 Anthu a mtundu wanu obalalitsidwawo akadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani ndi kukutengani kumeneko.+
6 “Fulumirani! Fulumirani anthu inu! Thawani m’dziko la kumpoto,”+ watero Yehova. “Anthu inu, ndinakubalalitsirani kutali kumbali zonse za dziko lapansi,”*+ watero Yehova.
31 Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwamphamvu kwa lipenga,+ ndipo adzasonkhanitsa osankhidwa ake+ kuchokera kumphepo zinayi,+ kuchokera kumalekezero a m’mlengalenga mpaka kumalekezero ena.