Yesaya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+ Yesaya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+ monga mmene panalili msewu umodzi umene Aisiraeli anayendamo m’tsiku limene anatuluka m’dziko la Iguputo. Yeremiya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Tsoka lidzamasulidwa kuchokera kumpoto ndipo lidzagwera anthu onse okhala m’dzikoli.+
12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+
16 Padzakhala msewu waukulu+ wochokera kudziko la Asuri woti mudzadutse anthu ake amene adzatsale,+ monga mmene panalili msewu umodzi umene Aisiraeli anayendamo m’tsiku limene anatuluka m’dziko la Iguputo.
14 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Tsoka lidzamasulidwa kuchokera kumpoto ndipo lidzagwera anthu onse okhala m’dzikoli.+