Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti adzalamula angelo ake za iwe,+Kuti akuteteze m’njira zako zonse.+ Salimo 91:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzakunyamula m’manja mwawo,+Kuti phazi lako lisawombe mwala uliwonse.+ Luka 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pajatu Malemba amati, ‘Iye adzalamula angelo ake za inu, kuti akutetezeni.’+ Luka 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho, ‘Adzakunyamulani m’manja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala uliwonse.’”+