Maliko 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poona izi, ena anakhumudwa ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani akuwononga chonchi mafuta onunkhirawa?+ Yohane 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yudasi Isikariyoti,+ mmodzi wa ophunzira ake, amene anali pafupi kumupereka anati:
4 Poona izi, ena anakhumudwa ndi kunena kuti: “N’chifukwa chiyani akuwononga chonchi mafuta onunkhirawa?+