Mateyu 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ophunzira ake ataona zimenezi anakwiya n’kunena kuti: “N’kuwonongeranji chonchi?+ Yohane 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yudasi Isikariyoti,+ mmodzi wa ophunzira ake, amene anali pafupi kumupereka anati: