Maliko 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithu ndikukuuzani, Kulikonse kumene uthenga wabwino udzalalikidwe m’dziko lonse,+ anthu azidzanenanso zimene mayiyu wachita kuti azidzam’kumbukira.”+
9 Ndithu ndikukuuzani, Kulikonse kumene uthenga wabwino udzalalikidwe m’dziko lonse,+ anthu azidzanenanso zimene mayiyu wachita kuti azidzam’kumbukira.”+