Maliko 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zoona, Mwana wa munthu akuchokadi, monga Malemba amanenera za iye. Koma tsoka kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu! Zikanakhala bwino munthu ameneyu akanapanda kubadwa.”+ Yohane 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene ndinali nawo pamodzi, ndinali kuwayang’anira+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa. Ine ndawasunga moti palibe aliyense wa iwo amene wawonongeka+ kupatulapo mwana wa chiwonongeko,+ kuti malemba akwaniritsidwe.+
21 Zoona, Mwana wa munthu akuchokadi, monga Malemba amanenera za iye. Koma tsoka kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu! Zikanakhala bwino munthu ameneyu akanapanda kubadwa.”+
12 Pamene ndinali nawo pamodzi, ndinali kuwayang’anira+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa. Ine ndawasunga moti palibe aliyense wa iwo amene wawonongeka+ kupatulapo mwana wa chiwonongeko,+ kuti malemba akwaniritsidwe.+