Yobu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Liwonongeke tsiku limene ndinabadwa,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu wapangika m’mimba.’ Mateyu 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zoona, Mwana wa munthu akuchokadi, monga Malemba amanenera+ za iye, koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino munthu ameneyu akanapanda kubadwa.”
3 “Liwonongeke tsiku limene ndinabadwa,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu wapangika m’mimba.’
24 Zoona, Mwana wa munthu akuchokadi, monga Malemba amanenera+ za iye, koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino munthu ameneyu akanapanda kubadwa.”