Maliko 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iye ananena molimba mtima kuti: “Ngati kuli kufa, ine ndifa nanu limodzi, sindingakukaneni.” Ndipo ena onse anayamba kunenanso chimodzimodzi.+ Luka 22:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo iye anauza Yesu kuti: “Ambuye, ndine wokonzeka kupita nanu limodzi kundende kapena kufa nanu limodzi.”+
31 Koma iye ananena molimba mtima kuti: “Ngati kuli kufa, ine ndifa nanu limodzi, sindingakukaneni.” Ndipo ena onse anayamba kunenanso chimodzimodzi.+
33 Pamenepo iye anauza Yesu kuti: “Ambuye, ndine wokonzeka kupita nanu limodzi kundende kapena kufa nanu limodzi.”+