Mateyu 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Petulo anamuyankha kuti: “Ngakhale ena onse atathawa kukusiyani, ine ndekha sindingathawe!”+ Maliko 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Petulo anauza Yesu kuti: “Ngakhale ena onse atathawa kukusiyani, koma ine ndekha sindidzatero.”+ Yohane 13:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Petulo anafunsanso kuti: “Ambuye, n’chifukwa chiyani sindingakutsatireni padakali pano? Ndidzapereka moyo wanga chifukwa cha inu.”+
29 Ndiyeno Petulo anauza Yesu kuti: “Ngakhale ena onse atathawa kukusiyani, koma ine ndekha sindidzatero.”+
37 Petulo anafunsanso kuti: “Ambuye, n’chifukwa chiyani sindingakutsatireni padakali pano? Ndidzapereka moyo wanga chifukwa cha inu.”+