Mateyu 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Petulo anamuyankha kuti: “Ngakhale ena onse atathawa nʼkukusiyani, ine ndekha sindingathawe!”+
33 Koma Petulo anamuyankha kuti: “Ngakhale ena onse atathawa nʼkukusiyani, ine ndekha sindingathawe!”+