Maliko 14:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma wina mwa amene anaimirira chapafupi anasolola lupanga lake ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+ Luka 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Wina wa iwo anatemadi kapolo wa mkulu wa ansembe ndi kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Yohane 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Simoni Petulo, popeza anali ndi lupanga, analisolola ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe ndi kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Dzina la kapoloyo anali Makasi.
47 Koma wina mwa amene anaimirira chapafupi anasolola lupanga lake ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+
10 Pamenepo Simoni Petulo, popeza anali ndi lupanga, analisolola ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe ndi kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Dzina la kapoloyo anali Makasi.