Mateyu 26:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Koma wina mwa amene anali ndi Yesu anasolola lupanga lake n’kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+ Maliko 14:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma wina mwa amene anaimirira chapafupi anasolola lupanga lake ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+ Luka 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Wina wa iwo anatemadi kapolo wa mkulu wa ansembe ndi kuduliratu khutu lake lakumanja.+
51 Koma wina mwa amene anali ndi Yesu anasolola lupanga lake n’kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+
47 Koma wina mwa amene anaimirira chapafupi anasolola lupanga lake ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+