Mateyu 26:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Koma mmodzi mwa anthu amene anali ndi Yesu anasolola lupanga lake nʼkutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:51 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 89/1/1986, tsa. 24
51 Koma mmodzi mwa anthu amene anali ndi Yesu anasolola lupanga lake nʼkutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+