Luka 22:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Iwo anati: “Tifuniranjinso umboni wina?+ Apatu tadzimvera tokha kuchokera pakamwa pake.”+