Levitiko 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+ Yohane 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ayudawo anamuyankha kuti: “Tili ndi chilamulo ife,+ ndipo malinga ndi chilamulocho iyeyu ayenera kufa, chifukwa akudziyesa mwana wa Mulungu.”+
16 Wonyoza dzina la Yehova aziphedwa ndithu.+ Khamu lonse lizim’ponya miyala. Kaya ndi mlendo wokhala pakati panu kapena nzika, aziphedwa chifukwa chonyoza Dzinalo.+
7 Ayudawo anamuyankha kuti: “Tili ndi chilamulo ife,+ ndipo malinga ndi chilamulocho iyeyu ayenera kufa, chifukwa akudziyesa mwana wa Mulungu.”+