Mateyu 26:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Koma Yesu anangokhala chete.+ Chotero mkulu wa ansembe anati: “Ndikukulumbiritsa pali Mulungu wamoyo,+ utiuze ngati ndiwedi Khristu+ Mwana wa Mulungu!” Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa chifukwa chimenechi, Ayudawo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, anali kunenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana+ ndi Mulungu.
63 Koma Yesu anangokhala chete.+ Chotero mkulu wa ansembe anati: “Ndikukulumbiritsa pali Mulungu wamoyo,+ utiuze ngati ndiwedi Khristu+ Mwana wa Mulungu!”
18 Pa chifukwa chimenechi, Ayudawo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa kuwonjezera pa kuphwanya Sabata, anali kunenanso kuti Mulungu ndi Atate wake,+ kudziyesa wofanana+ ndi Mulungu.