Mateyu 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Poyankha, Simoni Petulo ananena kuti: “Ndinu Khristu,+ Mwana wa Mulungu wamoyo.”+ Luka 22:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 “Tiuze ngati ndiwe Khristu.”+ Koma iye anawayankha kuti: “Ngakhale ndikuuzeni, simukhulupirira.+ Yohane 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Ayuda anamuzungulira ndi kuyamba kumuuza kuti: “Utivutitsa maganizo mpaka liti? Ngati ndiwedi Khristu,+ tiuze mosapita m’mbali.”+
24 Choncho Ayuda anamuzungulira ndi kuyamba kumuuza kuti: “Utivutitsa maganizo mpaka liti? Ngati ndiwedi Khristu,+ tiuze mosapita m’mbali.”+