Yohane 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati ndakuuzani zinthu za padziko lapansi koma inu osakhulupirira, mudzakhulupirira bwanji ndikakuuzani zinthu zakumwamba?+ Yohane 8:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma popeza ine ndimanena zoona, simundikhulupirira.+
12 Ngati ndakuuzani zinthu za padziko lapansi koma inu osakhulupirira, mudzakhulupirira bwanji ndikakuuzani zinthu zakumwamba?+