Maliko 14:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+ Luka 22:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Anali kumuphimba kumaso ndi kumufunsa kuti: “Losera. Wakumenya ndani?”+
65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+