Luka 22:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Patapita kanthawi pang’ono, munthu wina anamuona ndi kunena kuti: “Iwenso uli m’gulu la ophunzira ake.” Koma Petulo anati: “Munthu iwe, si ine ayi.”+
58 Patapita kanthawi pang’ono, munthu wina anamuona ndi kunena kuti: “Iwenso uli m’gulu la ophunzira ake.” Koma Petulo anati: “Munthu iwe, si ine ayi.”+