Mateyu 26:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Atatuluka n’kupita kukanyumba kapachipata, mtsikana wina anamuzindikira ndi kuuza ena amene anali pafupi kuti: “Bambo awa anali limodzi ndi Yesu Mnazaretiyu.”+ Maliko 14:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Kumenekonso mtsikana wantchito atamuona, anayamba kuuzanso amene anali ataimirira chapafupi kuti: “Bambo awanso ali m’gulu la ophunzira ake.”+ Yohane 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+
71 Atatuluka n’kupita kukanyumba kapachipata, mtsikana wina anamuzindikira ndi kuuza ena amene anali pafupi kuti: “Bambo awa anali limodzi ndi Yesu Mnazaretiyu.”+
69 Kumenekonso mtsikana wantchito atamuona, anayamba kuuzanso amene anali ataimirira chapafupi kuti: “Bambo awanso ali m’gulu la ophunzira ake.”+
25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+