58 Patapita kanthawi pang’ono, munthu wina anamuona ndi kunena kuti: “Iwenso uli m’gulu la ophunzira ake.” Koma Petulo anati: “Munthu iwe, si ine ayi.”+
25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+