Luka 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Akakamaliza kumukwapula+ akamupha,+ koma tsiku lachitatu iye adzauka.”+ Yohane 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Pilato anatenga Yesu ndi kumukwapula.+