Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 50:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Msana wanga ndinaupereka kwa ondimenya, ndipo masaya anga+ ndinawapereka kwa ozula ndevu. Nkhope yanga sindinaitchinjirize kuti isachitidwe zinthu zamanyazi ndi kulavuliridwa.+

  • Mateyu 20:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+

  • Mateyu 27:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamenepo anawamasulira Baraba, koma analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akam’pachike.+

  • Maliko 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+

  • Luka 18:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Akakamaliza kumukwapula+ akamupha,+ koma tsiku lachitatu iye adzauka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena