Mateyu 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo,+ anamuvula chinsalu chija ndi kumuveka malaya ake akunja n’kupita naye kukamupachika.+ Yohane 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Pilato anatenga Yesu ndi kumukwapula.+
31 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo,+ anamuvula chinsalu chija ndi kumuveka malaya ake akunja n’kupita naye kukamupachika.+