Maliko 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo, anamuvula chovala chofiirira chija ndi kumuveka malaya ake akunja. Atatero anatuluka naye kupita kokamupachika.+
20 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo, anamuvula chovala chofiirira chija ndi kumuveka malaya ake akunja. Atatero anatuluka naye kupita kokamupachika.+