Mateyu 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo,+ anamuvula chinsalu chija ndi kumuveka malaya ake akunja n’kupita naye kukamupachika.+ Yohane 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo anamupereka kwa iwo kuti akamupachike.+ Tsopano Yesu anakhala m’manja mwawo.
31 Atamaliza kumuchitira zachipongwezo,+ anamuvula chinsalu chija ndi kumuveka malaya ake akunja n’kupita naye kukamupachika.+