Maliko 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+ Luka 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anamasula+ munthu woponyedwa m’ndende pa mlandu woukira boma ndi kupha munthu, amenenso anthuwo anapempha kuti amumasule. Koma Yesu anamupereka m’manja mwawo kuti zofuna zawo zichitike.+
15 Pamenepo Pilato, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo,+ anawamasulira Baraba. Ndipo atalamula kuti Yesu amukwapule, anamupereka kuti akamupachike.+
25 Iye anamasula+ munthu woponyedwa m’ndende pa mlandu woukira boma ndi kupha munthu, amenenso anthuwo anapempha kuti amumasule. Koma Yesu anamupereka m’manja mwawo kuti zofuna zawo zichitike.+