Mateyu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri.+ Mateyu 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye sali pano chifukwa wauka kwa akufa+ monga ananenera. Bwerani muone pamene anagona. Maliko 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwo akam’chitira chipongwe, kum’lavulira, kum’kwapula ndi kumupha, koma patapita masiku atatu, adzauka.”+ Luka 18:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Akakamaliza kumukwapula+ akamupha,+ koma tsiku lachitatu iye adzauka.”+ Machitidwe 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ameneyu Mulungu anamuukitsa tsiku lachitatu ndi kumulola kuonekera,+ 1 Akorinto 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiponso kuti anaikidwa m’manda,+ kenako anaukitsidwa+ tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+
23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri.+
34 Iwo akam’chitira chipongwe, kum’lavulira, kum’kwapula ndi kumupha, koma patapita masiku atatu, adzauka.”+