Maliko 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ophunzirawo sanali kumvetsa mawuwa, ndipo anali kuopa kumufunsa.+ Luka 9:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma ophunzirawo sanamvetsebe tanthauzo la mawu amenewa. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo kuti asazindikire, ndipo anaopa kumufunsa za mawu amenewa.+
45 Koma ophunzirawo sanamvetsebe tanthauzo la mawu amenewa. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo kuti asazindikire, ndipo anaopa kumufunsa za mawu amenewa.+