Luka 9:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma ophunzirawo sanamvetsebe tanthauzo la mawu amenewa. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo kuti asazindikire, ndipo anaopa kumufunsa za mawu amenewa.+ Yohane 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anadziwa+ kuti akufuna kumufunsa, choncho iye anawafunsa kuti: “Kodi mukufunsana nokhanokha zimenezi, chifukwa ndanena kuti, Kwa kanthawi simudzandiona, ndipo kwa kanthawi mudzandiona?
45 Koma ophunzirawo sanamvetsebe tanthauzo la mawu amenewa. Tanthauzo lake linabisika kwa iwo kuti asazindikire, ndipo anaopa kumufunsa za mawu amenewa.+
19 Yesu anadziwa+ kuti akufuna kumufunsa, choncho iye anawafunsa kuti: “Kodi mukufunsana nokhanokha zimenezi, chifukwa ndanena kuti, Kwa kanthawi simudzandiona, ndipo kwa kanthawi mudzandiona?