-
Yohane 16:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Yesu anadziwa kuti akufuna kumufunsa, choncho anawafunsa kuti: “Kodi mukufunsana zimenezi chifukwa ndanena kuti: ‘Kwa kanthawi simudzandiona, komanso kuti kwa kanthawi mudzandionaʼ?
-