Yohane 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anadziwa+ kuti akufuna kumufunsa, choncho iye anawafunsa kuti: “Kodi mukufunsana nokhanokha zimenezi, chifukwa ndanena kuti, Kwa kanthawi simudzandiona, ndipo kwa kanthawi mudzandiona?
19 Yesu anadziwa+ kuti akufuna kumufunsa, choncho iye anawafunsa kuti: “Kodi mukufunsana nokhanokha zimenezi, chifukwa ndanena kuti, Kwa kanthawi simudzandiona, ndipo kwa kanthawi mudzandiona?