Maliko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso anali kum’menya m’mutu ndi bango ndi kumulavulira, ndipo anali kugwada ndi kumuweramira.+ Yohane 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+
3 Pamenepo anayamba kubwera kwa iye ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!” Komanso anali kumumenya mapama.+