Maliko 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+ Luka 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Komanso mmodzi wa ochita zoipa amene anapachikidwa naye pamodziwo anayamba kumulankhulira zachipongwe+ kuti: “Kodi si iwe Khristu? Dzipulumutse wekha, limodzi ndi ife.”
32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+
39 Komanso mmodzi wa ochita zoipa amene anapachikidwa naye pamodziwo anayamba kumulankhulira zachipongwe+ kuti: “Kodi si iwe Khristu? Dzipulumutse wekha, limodzi ndi ife.”