Deuteronomo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 mtembo wake usakhale pamtengopo usiku wonse,+ koma uzionetsetsa kuti wamuika m’manda tsiku lomwelo, chifukwa aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa ndi Mulungu.+ Usaipitse nthaka yako imene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa.+ Maliko 15:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa m’Bungwe Lalikulu la Ayuda, amenenso anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu,+ anapita kwa Pilato molimba mtima kukapempha mtembo+ wa Yesu. Luka 23:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Iye anapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.+
23 mtembo wake usakhale pamtengopo usiku wonse,+ koma uzionetsetsa kuti wamuika m’manda tsiku lomwelo, chifukwa aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa ndi Mulungu.+ Usaipitse nthaka yako imene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa.+
43 Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa m’Bungwe Lalikulu la Ayuda, amenenso anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu,+ anapita kwa Pilato molimba mtima kukapempha mtembo+ wa Yesu.