Mateyu 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+ Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anawayankha kuti: “Gwetsani kachisi uyu,+ ndipo ine ndidzamumanga m’masiku atatu.”
40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+