Luka 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndi wosayeneranso ngakhale kuuthira m’nthaka kapena m’manyowa. Anthu amangoutaya kunja. Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+
35 Ndi wosayeneranso ngakhale kuuthira m’nthaka kapena m’manyowa. Anthu amangoutaya kunja. Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+