Aefeso 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwiyani, koma musachimwe.+ Dzuwa lisalowe muli chikwiyire,+ Akolose 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma tsopano zonsezo muzitaye kutali ndi inu.+ Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa, ndi mawu achipongwe,+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+ Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+ Yakobo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwaweruza ndi kupha munthu wolungama. Iye akukutsutsani.+
8 Koma tsopano zonsezo muzitaye kutali ndi inu.+ Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa, ndi mawu achipongwe,+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+