Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 12:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Mwachitsanzo, pamene wokusumira mlandu akupita nawe kwa wolamulira, yesetsa kuchitapo kanthu muli m’njira, kuti uthetse mlanduwo. Uchitepo kanthu kuti asakutengere kwa woweruza, ndi kutinso woweruzayo asakupereke kwa msilikali wa pakhoti, ndipo msilikaliyo n’kukuponya m’ndende.+

  • Luka 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma mumzindawo munali mkazi wina wamasiye ndipo anali kupitapita+ kwa woweruza uja kukamupempha kuti, ‘Ndiweruzireni mlandu wanga ndi munthu amene akutsutsana nane, kuti pachitike chilungamo.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena