Luka 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene wakumenya patsaya ili,+ um’patsenso linalo. Amene wakulanda+ malaya ako akunja, usamuletse kutenga malaya ako amkati. 1 Akorinto 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena zoona, ndiye kuti mwalephereratu ngati mukutengerana kukhoti.+ Bwanji osangolola kulakwiridwa?+ Bwanji osalola kuberedwa?+
29 Amene wakumenya patsaya ili,+ um’patsenso linalo. Amene wakulanda+ malaya ako akunja, usamuletse kutenga malaya ako amkati.
7 Kunena zoona, ndiye kuti mwalephereratu ngati mukutengerana kukhoti.+ Bwanji osangolola kulakwiridwa?+ Bwanji osalola kuberedwa?+