Luka 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina a m’dzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti zinthu zonsezi n’zofunika kwa inu.+
30 Pakuti zonsezi ndi zinthu zimene anthu a mitundu ina a m’dzikoli amazifunafuna mwakhama, koma Atate wanu amadziwa kuti zinthu zonsezi n’zofunika kwa inu.+