Miyambo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Maso ako aziyang’ana patsogolo.+ Maso ako owala aziyang’anitsitsa patsogolo pako.+ Luka 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako lili lolunjika pa chinthu chimodzi, thupi lako lonse limawala kwambiri.+ Koma ngati lili loipa, thupi lako limachita mdima. Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+
34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako lili lolunjika pa chinthu chimodzi, thupi lako lonse limawala kwambiri.+ Koma ngati lili loipa, thupi lako limachita mdima.
18 Popeza maso+ a mtima wanu aunikiridwa,+ ndikukutchulanibe m’mapemphero anga kutinso mudziwe chiyembekezo+ chimene anakuitanirani, chuma chaulemerero+ chimene wasungira oyera monga cholowa,+