Luka 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako likuyangʼana* pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhalanso lowala kwambiri. Koma ngati lili ladyera,* thupi lako lonse lidzachitanso mdima.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:34 Nsanja ya Olonda,8/15/1988, ptsa. 8-9
34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako likuyangʼana* pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhalanso lowala kwambiri. Koma ngati lili ladyera,* thupi lako lonse lidzachitanso mdima.+