22 Nyale ya thupi ndi diso.+ Choncho ngati diso lako likuyangʼana pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhala lowala kwambiri. 23 Koma ngati diso lako lili ladyera,+ thupi lako lonse lidzachita mdima. Choncho ngati kuwala kumene kuli mwa iwe ndi mdima, ndiye kuti mdimawo ndi wandiweyani!