Miyambo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Maso ako aziyangʼana patsogolo.Inde, uziyangʼanitsitsa* zinthu zimene zili patsogolo pako.+ Luka 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako likuyangʼana* pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhalanso lowala kwambiri. Koma ngati lili ladyera,* thupi lako lonse lidzachitanso mdima.+ Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mulungu watsegula mitima yanu nʼcholinga choti muone komanso mudziwe chiyembekezo chimene wakupatsani ndiponso zinthu zabwino kwambiri zimene walonjeza kwa oyera,+
34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako likuyangʼana* pachinthu chimodzi, thupi lako lonse lidzakhalanso lowala kwambiri. Koma ngati lili ladyera,* thupi lako lonse lidzachitanso mdima.+
18 Mulungu watsegula mitima yanu nʼcholinga choti muone komanso mudziwe chiyembekezo chimene wakupatsani ndiponso zinthu zabwino kwambiri zimene walonjeza kwa oyera,+