Ezekieli 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+ 1 Akorinto 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.
13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+
13 ntchito ya wina aliyense idzaonekera. Pakuti tsikulo lidzasonyeza ntchitoyo poyera, chifukwa moto ndiwo udzaonetsa zimenezo poyera,+ ndipo motowo udzaonetsa kuti ntchito ya munthu aliyense ndi yotani.