Maliko 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kumenekonso munthu wina wakhate anafika kwa iye, ndipo anagwada pansi ndi kum’dandaulira, kuti: “Ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+ Luka 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi inanso pamene anali mumzinda wina, anakumana ndi munthu wakhate thupi lonse. Pamene anaona Yesu, munthuyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kum’pempha, kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
40 Kumenekonso munthu wina wakhate anafika kwa iye, ndipo anagwada pansi ndi kum’dandaulira, kuti: “Ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
12 Nthawi inanso pamene anali mumzinda wina, anakumana ndi munthu wakhate thupi lonse. Pamene anaona Yesu, munthuyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kum’pempha, kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+