Mateyu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.” Luka 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi inanso pamene anali mumzinda wina, anakumana ndi munthu wakhate thupi lonse. Pamene anaona Yesu, munthuyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kum’pempha, kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”
12 Nthawi inanso pamene anali mumzinda wina, anakumana ndi munthu wakhate thupi lonse. Pamene anaona Yesu, munthuyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kum’pempha, kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+